Muubwezi muli ngati pasukulu
Zambiri tiphunzira kwa athu okondedwa
Nkhawa kumachotsa ndi ndi chikondi Cha okondedwa
Pena nakhumudwa ndi athu okondedwa
Poti muliso malamulo muubwezi
Muubwezi sindufunika mwano
Akafunsa wako okondedwa osayankha mwa mwano
Inde muubwezi mmafunika ngati Cha nyerere chi mvano
Kudzichepetsa ndilo gwero lokhalitsa kwa ubwezi
Kudzimva ndi mwano ndizo zithetsa ubwezi
Muubwezi tipezamoso mtendere
Tipezaso chisamalirk ngati Cha Mai wa mtendere
Bola ngati kumvana kulipo
Eya bola ngatiso kupilira kulipo
Mwanoso ndi kunyada ngati sukukhalapo