Sukulu yathu ndiyabwino

Pali zinthu zabwino

Zinthu zimayenda bwino

Anthuso ake ndi a khalidwe labwino

Sukulu yathu yathu iyi

Palibe zachibwana ai

Kusuta fodya ndi kumwa mowa samalorai

Tikunena Rumphi TTC osati ina ai

Pasukulu yathu yabwino

Pali aphunzitsi Abwino

Inde ochotsa umbuli bwino

Dzaoneni nawo sukulu yabwino

Pasukulu yathu ngati wa njerere Pali umodzi

Pazilizose ngati ngumbi zothothola mapiko timakhala limodzi

Inde timamvana chimodzi

Podziwa kuti tonse ndife amodzi