Ndayima Pano pa chulu,maso anga opendekera uko kusapitwa.
Ndayima Pano maso anga kupenyera uko kuli anasi a mtima ofewa anapita.
Ndayima pa phiri chikondi kuzizwa ndi mawu amphamvu omwe awo ananena.
Ndayima Pano kuyamika iwo anatenga mikondo kumenyana ndi asamunda.