Kodi umandikonda? Ndiyankhe pompano
Umaganiza za ine nthawi zose? Tayankha pompano
Zochita zako pena sindimazimvetsa
Chikondi chako simachimvetsa
Kodi umandikonda?
Dzulo ndakupeza ndi munthu Wina
Ntakuufusa amayankha Zina
Kodi unapeza Wina?
Kodi umandikonda?
Zeni zeni ndiuze namwaliwe
Sindufuna patsogolo pano ndzalire
Ndikufuna mpaka kale ndzakusamalire